Tingakumane bwanji ndi Gwamba Ku kasungu?
STEP 1
muonetsetse kut ndinu artist, producer or a designer
GWAMBA wayankhula pa kasungu community radio pa program ya pachikhona lachitatu kut week yamawa (date not announced yet) azakhala Ali KU KASUNGU stadium ndi ma artist akuluakulu monga.. Kell Kay, Charisma, BFB ndiena ambili.. Gwamba watsimikiza kuti akakhala akucheza ndi ma artist amukakusungu mmomwe angaphushiri music patsogolo. Komaso akakumana ndi ma designers amukasungu ndikuwa phuzitsa mene angakapangile improve ma products awo
STEP 2
Ukuyenela kuzikozekeletsa to meet up the landlord.. ukuyenela ku traina' ti ma freestyle komaso follow the procedures omwe mutauzidwe
STEP 3
pitani pa Facebook mupange search and like page yoti or click👉 Biz Savetor the Blogger🤗kuti muziwe zotsatila zambili ndi date yomwe mutakakumane ndi a gwambuzi
STEP 4
mumuuze Gwamba kut ma blogger so akumane nafe hahah lol Have a blessed time . Read more stories on my blogspot
Comments